Nations Bible

1 Crónicas 2

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · Toca un versículo para ver sus referencias cruzadas.

Ana a Israeli

1Ana a Israeli anali awa:

Rubeni, Simeoni, Levi, Yuda, Isakara, Zebuloni, 2Dani, Yosefe, Benjamini, Nafutali, Gadi ndi Aseri.

Yuda Mpaka pa Ana a Hezironi

Ana a Hezironi

3Ana a Yuda anali awa:

Eri, Onani ndi Sela. Ana atatu awa anabereka ndi mkazi wa Chikanaani, Batisuwa. Eri, mwana woyamba wa Yuda anali woyipa kwambiri pamaso pa Yehova, kotero Yehova anamupha. 4Mpongozi wake Tamara anamuberekera Perezi ndi Zera. Ana onse a Yuda analipo asanu.

5Ana a Perezi anali awa:

Hezironi ndi Hamuli.

6Ana a Zera anali awa:

Zimuri, Etani, Hemani, Kalikoli ndi Dara. Onse analipo asanu.

7Mwana wa Karimi anali

Akani, amene anabweretsa mavuto pakati pa Israeli pamene anatenga zinthu zoyenera kuwonongedwa.

8Mwana wa Etani anali

Azariya.

9Ana amene anabadwa kwa Hezironi anali:

Yerahimeeli, Ramu ndi Kelubai.

Kuchokera kwa Ramu Mwana wa Hezironi

10Ramu anabereka

Aminadabu ndipo Aminadabu anali abambo ake a Naasoni, mtsogoleri wa fuko la Yuda. 11Naasoni anabereka Salima, Salima anabereka Bowazi, 12Bowazi anabereka Obedi ndipo Obedi anabereka Yese.

13Yese anabereka

Eliabu mwana wake woyamba, wachiwiri Abinadabu, wachitatu Simea, 14wachinayi Netaneli, wachisanu Radai, 15wachisanu ndi chimodzi Ozemu ndi wachisanu ndi chiwiri Davide. 16Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli. Ana atatu a Zeruya anali Abisai Yowabu ndi Asaheli. 17Abigayeli anali amayi ake a Amasa amene abambo ake anali Yeteri wa fuko la Ismaeli.

Kalebe Mwana wa Hezironi

18Kalebe mwana wa Hezironi anabereka ana mwa Azuba mkazi wake (ndi mwa Yerioti). Ana a mkaziyo anali awa: Yeseri, Sobabu ndi Aridoni. 19Azuba atamwalira, Kalebe anakwatira Efurata, amene anamuberekera Huri. 20Huri anabereka Uri ndipo Uri anabereka Bezaleli.

21Patapita nthawi, Hezironi anagona ndi mwana wamkazi wa Makiri abambo ake a Giliyadi (iye anamukwatira ali ndi zaka 60) ndipo anamuberekera Segubu. 22Segubu anabereka Yairi, amene anali ndi mizinda 23 ku Giliyadi. 23(Koma Gesuri ndi Aramu analanda Havoti Yairi komanso Kenati ndi madera ake onse ozungulira, mizinda makumi asanu ndi umodzi). Onsewa anali adzukulu, a Makiri abambo ake a Giliyadi.

24Atamwalira Hezironi ku Kalebe Efurata, Abiya mkazi wa Hezironi anamuberekera Asihuri abambo a Tekowa.

Yerahimeeli Mwana wa Hezironi

25Ana a Yerahimeeli, mwana woyamba wa Hezironi anali:

Ramu, mwana wake woyamba, Buna, Oreni, Ozemu ndi Ahiya. 26Yerahimeeli anali ndi mkazi wina amene dzina lake linali Atara, amene anali amayi a Onamu.

27Ana a Ramu, mwana woyamba wa Yerahimeeli, anali awa:

Maazi, Yamini ndi Ekeri.

28Ana a Onamu anali awa:

Shamai ndi Yada.

Ana a Shamai anali awa:

Nadabu ndi Abisuri.

29Mkazi wa Abisuri anali Abihaili, amene anamuberekera Ahibani ndi Molidi.

30Ana a Nadabu anali awa:

Seledi ndi Apaimu. Koma Seledi anamwalira wopanda ana.

31Ana a Apaimu anali awa:

Isi, amene anabereka Sesani.

Sesani anabereka Ahilai.

32Ana a Yada, mʼbale wa Samai, anali awa:

Yereri ndi Yonatani. Koma Yeteri anamwalira wopanda ana.

33Ana a Yonatani anali awa:

Peleti ndi Zaza.

Amenewa anali adzukulu a Yerahimeeli.

34Sesani sanabereke ana aamuna koma aakazi okhaokha.

Iye anali ndi wantchito wa ku Igupto, dzina lake Yariha. 35Sesani anapereka mwana wake wamkazi kwa Yariha wantchito wake kuti amukwatire ndipo anamuberekera Atayi.

36Atayi anali abambo ake a Natani,

Natani anali abambo ake a Zabadi,

37Zabadi anali abambo a Efilali,

Efilali anali abambo a Obedi,

38Obedi anali abambo a Yehu,

Yehu anali abambo a Azariya,

39Azariya anali abambo a Helezi,

Helezi anali abambo a Eleasa,

40Eleasa anali abambo ake a Sisimai,

Sisimai anali abambo a Salumu,

41Salumu anali abambo a Yekamiya,

Yekamiya anali abambo a Elisama.

Mabanja a Kalebe

42Ana a Kalebe mʼbale wa Yerahimeeli anali awa:

Mesa mwana wachisamba, anali abambo a Zifi, ndipo mwana wake Maresa anali abambo a Hebroni.

43Ana a Hebroni anali awa:

Kora, Tapuwa, Rekemu ndi Sema. 44Sema anali abambo ake Rahamu ndipo Rahamu anali abambo a Yorikeamu. Rekemu anali abambo a Samai. 45Mwana wa Samai anali Maoni, ndipo Maoni anali abambo a Beti Zuri.

46Efai, mzikazi wa Kalebe, anali amayi a Harani, Moza ndi Gazezi. Harani anali abambo a Gazezi.

47Ana a Yahidai anali awa:

Regemu, Yotamu, Gesani, Peleti, Efai ndi Saafi.

48Maaka mzikazi wa Kalebe anali mayi Seberi ndi Tirihana. 49Iye anaberekanso Saafi abambo a Madimena ndi Seva abambo a Makibena ndi Gibeya. Mwana wamkazi wa Kalebe anali Akisa. 50Izi zinali zidzukulu za Kalebe.

Ana a Huri mwana wachisamba wa Efurata anali awa:

Sobala abambo a Kiriati Yearimu, 51Salima abambo a Betelehemu ndi Harefu abambo ake a Beti-Gadera.

52Zidzukulu za Sobala abambo a Kiriati Yearimu zinali izi:

Harowe, theka la banja la Manahati, 53ndipo mabanja a Kiriati-Yeyarimu anali awa: Aitiri, Aputi, Asumati ndi Amisirai. Azorati ndi Aesitaoli anachokera kwa amenewa.

54Zidzukulu za Salima zinali izi:

Betelehemu, Anetofati, Atiroti-Beti-Yowabu, theka la banja la Manahati, Azori, 55ndiponso mabanja a alembi amene amakhala ku Yabesi: Atiroti, Asimeati ndiponso Asukati. Awa ndi Akeni amene anachokera kwa Hamati, kholo la Arekabu.

Ilustración artística: una interpretación, no un registro histórico.

¿Sabías que…?

La genealogía de Judá y la línea real

  • El linaje en este capítulo traza la descendencia de Judá a través de Fares y Hezrón hasta Ram, culminando en David, el séptimo hijo de Isaí. Esta línea destaca antepasados notables, incluidos Naasón, un líder de la tribu durante la travesía por el desierto, y Booz de Belén.Fuentes: el propio texto bíblico · Nahshon · Boaz · Ram
  • Las genealogías en 1 Crónicas a menudo vinculan familias directamente con los asentamientos que establecieron. Los descendientes de Caleb, hijo de Hezrón, y de su nieto Hur son identificados como padres o fundadores de ciudades destacadas de Judá como Belén, Quiriat-jearim y Madmana.Fuentes: el propio texto bíblico · Caleb · Madmannah
  • Cuando Sesán, de la rama de Jerameel, no tuvo hijos varones, preservó su linaje casando a su hija con su siervo egipcio Jarha, cuyos descendientes se registran a lo largo de trece generaciones.Fuentes: el propio texto bíblico

Notas escritas con ayuda de IA a partir de fuentes abiertas (Theographic Bible Metadata, CC BY-SA 4.0; Easton’s Bible Dictionary, dominio público) y revisadas antes de publicarse.

Lugares de este capítulo

  • Gilead · Hoy: Gilead 1 · 32.187, 35.692 · versículo 22
  • Aram · 33.511, 36.306 · versículo 23
  • Geshur · 32.767, 35.700 · versículo 23
  • Havvoth-jair · 32.588, 35.726 · versículo 23
  • Tekoa · Hoy: Khirbet Teku’a · 31.632, 35.210 · versículo 24
  • Kiriath-jearim · Hoy: Deir el Azar · 31.809, 35.104 · versículos 50, 52, 53
  • Bethlehem · 31.704, 35.208 · versículos 51, 54

Solo aparecen lugares identificados con alta confianza (90 % o más según las fuentes académicas reunidas por OpenBible). Mapa de la época: DARE (Digital Atlas of the Roman Empire), CC BY 4.0; mapa actual: © colaboradores de OpenStreetMap; lugares: OpenBible.info (CC BY 4.0).

Créditos y licencia de esta traducción
Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
The Holy Bible in the Chichewa language of Malawi: Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
copyright © 2016, 2002 Biblica, Inc.
Language: Chichewa
Contributor: Biblica, Inc.
Ntchito ino imapezeka pansi pa Creative Commons Attribution –ShareAlike 4.0 Chilolezo cha Ponseponse (CC BY-SA). Mukafuna kuona chilolezo chimenechi, pitani pa http://creativecommons.org/licenses/by-sa/4‪.0 kapena lembani kalata ku Creative Commons, PO Box 1866, Mountain View, CA 94042, USA.
Biblica® ndicho chizindikiro choikidwa ndi Biblica ndipo kuti mugwiritse ntchito Biblica® pafunika chilolezo cholembedwa ndi Biblica, Inc. mwini wake. Pansi pa malamulo a chilolezo cha CC BY-SA, mukhoza kukopa ndi kugawira ena ntchitoyi, mosaisintha pokhapokha ngati mukusunga chizindikiro cha Biblica® mosamala ndi mosachisintha. Mukafuna kusintha ntchitoyi kapena kuitanthauzira m’njira inayake, muyenera kuchotsa chizindikiro ichi cha Biblica®. Mukasintha, onetsani bwinobwino zimene mwasinthazo ndipo dziwitsani kuti: “Ntchito yonse ya Biblica, Inc. imene mwatengapo kagawo chabe ikupezeka mwaulere pa www.biblica.com ndi pa open.bible.”
Chidziwitso cha umwini chiyenera kuoneka pa tsamba lonena za Mutu wa Nchitoyi kapena pa tsamba lapadera lonena za umwini wa ntchitoyi motere:
Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™
Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.
Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™
Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.
“Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo.
“Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.\m Ntchito mwaichitayo ichitike potsatira malamulo a chilolezo chija (CC BY-SA).
Mukafuna kudziwitsa Biblica, Inc. zokhudza matanthauzidwe anu a ntchitoyi, chonde tipezeni pa https://open.bible/contact-us.
This work is made available under the Creative Commons Attribution-ShareAlike 4‪.0 International License (CC BY-SA). To view a copy of this license, visit http://creativecommons.org/licenses/by-sa/4‪.0 or send a letter to Creative Commons, PO Box 1866, Mountain View, CA 94042, USA.
Biblica® is a trademark registered by Biblica, Inc., and use of the Biblica® trademark requires the written permission of Biblica, Inc. Under the terms of the CC BY-SA license, you may copy and redistribute this unmodified work as long as you keep the Biblica® trademark intact. If you modify a copy or translate this work, thereby creating a derivative work, you must remove the Biblica® trademark. On the derivative work, you must indicate what changes you have made and attribute the work as follows: “The original work by Biblica, Inc. is available for free at www.biblica.com and open.bible.”
Notice of copyright must appear on the title or copyright page of the work as follows:
Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™
Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.
Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™
Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.
“Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo.
“Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.\m You must also make your derivative work available under the same license (CC BY-SA).
‪If you would like to notify Biblica, Inc. regarding your translation of this work, please contact us at https://open.bible/contact-us.
This translation is made available to you under the terms of the
Creative Commons Attribution Share-Alike license 4.0.
You have permission to share and redistribute this Bible translation in any format and to make reasonable revisions and adaptations of this translation, provided that:
You include the above copyright and source information.
If you make any changes to the text, you must indicate that you did so in a way that makes it clear that the original licensor is not necessarily endorsing your changes.
If you redistribute this text, you must distribute your contributions under the same license as the original.
Pictures included with Scriptures and other documents on this site are licensed just for use with those Scriptures and documents.
For other uses, please contact the respective copyright owners.
Note that in addition to the rules above, revising and adapting God's Word involves a great responsibility to be true to God's Word. See Revelation 22:18-19.
2025-05-20

Fuente: http://ebible.org/nya/ · eBible.org

Habla con nosotros

Cuéntanos desde dónde lees, cómo te ha ayudado la Biblia o qué podemos mejorar. Leemos todos los mensajes.